Job 30:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ndikudziŵa kuti Inu mudzandifikitsa ku imfa yanga, kumene aliyense adzapitako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ndidziwa kuti mudzandifikitsa kuimfa, ndi kunyumba yokomanamo amoyo onse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndikudziwa kuti Inu mudzandifikitsa ku imfa, kumalo kumene amoyo onse adzapitako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ndidziwa kuti mudzandifikitsa kuimfa, Ndi ku nyumba yokomanamo amoyo onse.