Job 30:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi ine sindidalire nawo anzanga amene anali pa mavuto? Kodi mtima wanga sudaŵamvere chisoni anthu osauka?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi sindinamlirira misozi wakulawa zowawa? Kodi moyo wanga sunachitira chisoni osowa?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi ine sindinalire nawo iwo amene anali pamavuto? Kodi mtima wanga sunamvere chisoni anthu osauka?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi sindinamlirira misozi wakulawa zowawa? Kodi moyo wanga sunacitira cisoni osowa?