Job 30:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma pamene ndinkayembekeza zabwino, zovuta ndiye zimene zidandigwera. Pamene ndinkayembekeza kuŵala, mdima ndi umene udandiphimba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Muja ndinayembekeza chokoma chinadza choipa, ndipo polindira kuunika unadza mdima.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma pamene ndinkayembekezera zabwino, zoyipa ndiye zinandigwera; pamene ndinkafunafuna kuwala, mdima ndiye unandigwera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Muja ndinayembekeza cokoma cinadza coipa, Ndipo polindira kuunika unadza mdima.