Job 30:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtima wanga ukuŵaŵa, ndikusoŵa mpumulo, masiku onse ndili pa mavuto.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
M'kati mwanga mupweteka mosapuma, masiku a mazunzo andidzera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuwawa kwa mʼkati mwanga sikukuleka; ndili mʼmasiku amasautso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
M'kati mwanga mupweteka mosapuma, Masiku a mazunzo andidzera.