Job 30:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kulira kwanga kuli ngati kwa nkhandwe, ndimakhala ndekha ngati nthiŵatiŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndili mbale wao wa ankhandwe, ndi mnansi wao wa nthiwatiwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndasanduka mʼbale wa nkhandwe, mnzawo wa akadzidzi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiri mbale wao wa ankhandwe, Ndi mnansi wao wa nthiwatiwa.