Job 30:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anali atatheratu kuwonda ndi njala, natsala mafupa okhaokha, ankakungudza nthaka youma yachipululu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
atsala mafupa okhaokha ndi kusowa ndi njala; akungudza nthaka youma kuli mdima wa m'chipululu chopasuka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anali atatheratu kuwonda ndi njala, ankayendayenda mʼdziko lopanda madzi, mʼchipululu usiku.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Atsala mafupa okha okha ndi kusowa ndi njala; Akungudza nthaka youma kuli mdima wa m'cipululu copasuka.