Job 30:31 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pangwe wanga wasanduka woimbira maliro, chitoliro changa chikupolokeza anthu olira.” Yobe avomera kuchimwa kwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake zeze wanga wasandulika wa maliro, ndi chitoliro changa cha mau a olira misozi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pangwe wanga wasanduka woyimbira maliro, ndipo chitoliro changa chikuyimbira anthu olira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace zeze wanga wasandulika wa maliro, Ndi citoliro canga ca mau a olira misozi.