Job 30:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ankathyola therere ndi masamba a zitsamba, ankadya mizu ya dinde.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Atchera therere lokolera kuzitsamba, ndi chakudya chao ndicho mizu ya dinde.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ankathyola therere ndi masamba owawa, ndipo chakudya chawo chinali mizu ya mitengo ya masache.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Achera terere lokolera kuzitsamba, Ndi cakudya cao ndico mizu ya dinde.