Job 30:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ankaŵapirikitsa pakati pa anthu, anzao ankaŵakuwa ngati mbala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anawapirikitsa pakati pa anthu, awafuulira ngati kutsata mbala.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anapirikitsidwa pakati pa anthu anzawo, akuwakuwiza ngati kuti anali akuba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anawapitikitsa pakati pa anthu, Awapfuulira ngati kutsata mbala.