Job 30:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ankaumirizidwa kumakhala m'zigwembe za mitsinje, m'maenje am'nthaka ndi am'matanthwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Azikhala m'zigwa za chizirezire, m'maenje a m'nthaka ndi m'mapanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anawumirizidwa kukhala ku zigwembe za mitsinje yowuma, pakati pa matanthwe ndi mʼmaenje a mʼnthaka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Azikhala m'zigwa za cizirezire, M'maenje a m'nthaka ndi m'mapanga.