Job 30:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ankalira ngati nyama kuthengo, ndipo ankaunjikana pamodzi pa zitsamba zaminga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakati pa zitsamba alira ngati bulu, pansi pa khwisa asonkhana pamodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ankalira ngati nyama kuthengo ndipo ankawunjikana pamodzi pa ziyangoyango.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakati pa zitsamba alira ngati buru, Pansi pa khwisa asonkhana pamodzi.