Job 30:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwowo anali opusa, achabechabe okhaokha, ndipo adaŵachotsa m'dziko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndiwo ana a opusa, inde ana a anthu opanda dzina; anawaingitsa kuwachotsa m'dziko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anali anthu achabechabe ndi wopanda dzina, anathamangitsidwa mʼdziko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiwo ana a opusa, inde ana a anthu opanda dzina; Anawaingitsa kuwacotsa m'dziko.