Job 31:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kuipa kwake kukadakhala ngati moto woonongeratu, ukadapsereza zinthu zanga zonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ndicho moto wakunyeka mpaka chionongeko, ndi chakuzula zipatso zanga zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndi moto umene umayaka mpaka chiwonongeko; ukanapsereza zokolola zanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ndico moto wakunyeka mpaka cionongeko, Ndi cakuzula zipatso zanga zonse.