Job 31:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ngati ndidapondereza mlandu wa mtumiki wanga, wamwamuna kapena wamkazi, pamene adabwera kwa ine ndi madandaulo ake,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ngati ndapeputsa mlandu wa kapolo wanga, kapena wa mdzakazi wanga, potsutsana nane iwo,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ngati ndinkapondereza mlandu wa akapolo anga aamuna kapena aakazi, pamene ankabwera kwa ine ndi milandu yawo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati ndapeputsa mlandu wa kapolo wanga, kapena wa mdzakazi wanga, Potsutsana nane iwo,