Job 31:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ngati amphaŵi ndidaŵamana zimene ankakhumba, kapena kuŵagwiritsa mwala mwankhanza akazi amasiye,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ngati ndakaniza aumphawi chifuniro chao, kapena kutopetsa maso a amasiye,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ngati ndinawamana aumphawi zinthu zimene ankazikhumba, kapena kuwagwiritsa fuwa lamoto akazi amasiye amene amafuna thandizo kwa ine,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati ndakaniza aumphawi cifuniro cao, Kapena kutopetsa maso a amasiye,