Job 31:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ngati chakudya ndidadya ndekha, ana amasiye osachilaŵa,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kapena kudya nthongo yanga ndekha, osadyako mwana wamasiye;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ngati chakudya changa ndinadya ndekha, wosagawirako mwana wamasiye,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kapena kudya nthongo yanga ndekha, Osadyako mwana wamasiye;