Job 31:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
pakuti anawo ndidaŵalera ngati bambo wao ndi kuŵasamalira bwino chibadwire chao,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
(pakuti kuyambira ubwana wanga analeredwa ndi ine monga ndi atate; ndipo ndinakhala nkhoswe ya wamasiye chibadwire ine.)
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
chonsechotu kuyambira unyamata wanga ndinamulera monga abambo ake, ndipo moyo wanga wonse ndakhala ndikusamalira akazi amasiye,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
(Pakuti kuyambira ubwana wanga analeredwa ndi ine monga ndi atate; Ndipo ndinakhala nkhoswe ya wamasiye cibadwire ine.)