Job 31:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ngati ndidaona wina aliyense akuzunzika ndi usiŵa, kapena munthu wosauka alibe chofunda,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ngati ndinaona wina alinkutayika wopanda chovala, kapena kuti wosowa alibe chofunda;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ngati ndinaona wina aliyense akuzunzika ndi usiwa, kapena munthu wosauka alibe chofunda,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati ndinaona wina alinkutayika wopanda cobvala, Kapena kuti wosowa alibe copfunda;