Job 31:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi Mulungu kumwamba akadandisungira zotani? Kodi Mphambe kumwamba akadandikonzera zabwino zanji?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti gawo la Mulungu lochokera kumwamba, ndi cholowa cha Wamphamvuyonse chochokera m'mwambamo nchiyani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi Mulungu kumwambako wandisungira zotani? Kodi cholowa changa chochokera kwa Wamphamvuzonse kumwambako nʼchotani?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti gawo la Mulungu locokera kumwamba, Ndi colowa ca Wamphamvuyonse cocokera m'mwambamo nciani?