Job 31:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ngati iyeyo sadanditamande chifukwa chomupatsa chovala, ndipo ngati sindidamfunditsa ndi nsalu za ubweya wa nkhosa,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ngati ziuno zake sizinandiyamika, ngati sanafunde ubweya wa nkhosa zanga;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo ngati iyeyo sananditamandepo chifukwa chomufunditsa ndi nsalu ya ubweya wankhosa,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati zuuno zace sizinandiyamika, Ngati sanapfunda ubweya wa nkhosa zanga;