Job 31:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ngati ndidaopsezapo mwana wamasiye, podziŵa kuti ku bwalo lamilandu sadzanditsutsa,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ngati ndinasamulira ana amasiye dzanja langa, popeza ndinaona thandizo langa kuchipata;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ngati ndinaopsezapo mwana wamasiye, poganiza kuti ndinali ndi mphamvu mʼbwalo la milandu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati ndinasamulira ana amasiye dzanja langa, Popeza ndinaona thandizo langa kucipata;