Job 31:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakutitu tsoka lochokera kwa Mulungu ndimachita nalo mantha, sindikadatha kuchita kanthu kalikonse koipa pamaso pake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti tsoka lochokera kwa Mulungu linandiopsa, ndi chifukwa cha ukulu wake sindinakhoza kanthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Popeza ine ndinaopa kwambiri chiwonongeko chochokera kwa Mulungu, ndinachitanso mantha ndi ulemerero wake, sindikanatha kuchita zinthu zimenezi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti tsoka locokera kwa Mulungu linandiopsa, Ndi cifukwa ca ukulu wace sindinakhoza kanthu,