Job 31:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Sindidaike mtima pa chuma, kapena kudalira golide wabwino kwambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ngati ndayesa golide chiyembekezo changa, ndi kunena ndi golide woyengetsa, ndiwe chikhazikitso changa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ngati ndinayika mtima wanga pa chuma kapena kunena kwa golide wabwino kwambiri kuti, ‘Iwe ndiye chitetezo changa,’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati ndayesa golidi ciyembekezo canga, Ndi kunena ndi golidi woyengetsa, Ndiwe cikhazikitso canga;