Job 31:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zedi, sindidakondwere chifukwa choti chuma changa chinali chambiri, kapena chifukwa choti manja anga adapata zambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ngati ndinakondwera popeza chuma changa nchachikulu, ndi dzanja langa lapeza zochuluka;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ngati ndinakondwera chifukwa choti chuma changa chinali chambiri, zinthu zimene manja anga anazipeza,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati ndinakondwera popeza cuma canga ncacikuru, Ndi dzanja langa lapeza zocuruka;