Job 31:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Poona dzuŵa likuŵala, kapena mwezi ukuwonetsa kukongola kwake,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ngati ndalambira dzuwa lilikuwala, kapena mwezi ulikuyenda monyezimira;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ngati pamene ndinaona dzuwa likuwala, kapena mwezi ukuyenda mwa ulemerero wake,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati ndalambira dzuwa lirikuwala, Kapena mwezi ulikuyenda monyezimira;