Job 31:27 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
mtima wanga ukadakopeka nazo, dzanja langa nkuliika pakamwa mozilemekeza,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi mtima wanga wakopeka m'tseri, ndi pakamwa panga padapsompsona dzanja langa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo kuti mtima wanga unakopeka nazo nʼkuyika dzanja langa pakamwa mozilemekeza,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi mtima wanga wakopeka m'tseri, Ndi pakamwa panga padapsompsona dzanja langa;