Job 31:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
bwenzi limeneli lili tchimo loti aweruzi andilange nalo, chifukwa ndikadakhala wonama kwa Mulungu wakumwamba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ichinso ndi mphulupulu yoyenera oweruza kunena mlandu wake; pakuti ndikadakana Mulungu ali m'mwamba.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pamenepo zimenezinso zikanakhala machimo oti ndilangidwe nawo, chifukwa ndikanakhala wosakhulupirika kwa Mulungu wakumwamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Icinso ndi mphulupulu yoyenera oweruza kunena mlandu wace; Pakuti ndikadakana Mulungu ali m'mwamba.