Job 31:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Sindidakondwerere kuwonongeka kwa mdani wanga. Sindidasekere tsoka litamgwera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ngati ndakondwera nalo tsoka la wondida, kapena kudzitukula pompeza choipa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ngati ndinasangalala ndi kuwonongeka kwa mdani wanga, kapena kusekera mavuto pamene mavuto anamugwera,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati ndakondwera nalo tsoka la wondida, Kapena kudzitukula pompeza coipa;