Job 31:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sindidachimwe ndi pakamwa panga, potemberera mdani wanga kuti aonongeke.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndithu sindinalola m'kamwa mwanga muchimwe, kupempha motemberera moyo wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ine sindinachimwe ndi pakamwa panga potulutsa matemberero a mdani wanga kuti awonongeke,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndithu sindinalola m'kamwa mwanga mucimwe, Kupempha motemberera moyo wace.