Job 31:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu ena amabisa zoipa zao, koma ine sindidabise cholakwa chilichonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ngati ndakwirira zolakwa zanga monga Adamu, ndi kubisa mphulupulu yanga m'chifuwa mwanga;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ngati ndinabisa tchimo langa monga amachitira anthu ena, kubisa kulakwa mu mtima mwanga
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati ndakwirira zolakwa zanga monga Adamu, Ndi kubisa mphulupulu yanga m'cifuwa mwanga;