Job 31:36 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
ndikadachita kuipachika kalatayo paphewa panga monyadira, ndikadaivalanso kumutu ngati chisoti chaufumu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndithu ndikadawasenza paphewa panga, ndi kudzimangirira awa ngati korona.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndithu ine ndikanakoleka kalatayo pa phewa langa, ndikanayivala kumutu ngati chipewa chaufumu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndithu ndikadawasenza paphewa panga, Ndi kudzimangirira awa ngati korona.