Job 31:38 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ngati ndidalanda minda ya anthu ena osagula, ngati ndikulima pa minda ya eniake,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ngati minda yanga ifuula monditsutsa, ndi nthumbira zake zilira pamodzi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ngati minda yanga ikulira monditsutsa ine ndipo malo ake onse osalimidwa anyowa ndi misozi,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati minda yanga ipfuula monditsutsa, Ndi nthumbira zace zilira pamodzi;