Job 31:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Sindidachite zachiphamaso, sindidayesepo kunyenga anthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ngati ndinayanjana nalo bodza, ndi phazi langa linathamangira chinyengo;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ngati ndachita zinthu mwachiphamaso, kapena kufulumira kukachita zachinyengo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati ndinayanjana nalo bodza, Ndi phazi langa linathamangira cinyengo;