Job 31:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngati mayendedwe anga asempha njira, ngati mtima wanga wakhumbira zinthu molakwa, ndipo ngati ndachita choipa chilichonse,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ngati phazi langa linapatuka m'njira, ndi mtima wanga unatsata maso anga? Ngati chilema chamamatira manja anga?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ngati mayendedwe anga asempha njira, ngati mtima wanga wakhumbira zimene maso anga aona, kapena ngati ndachita choyipa chilichonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati phazi langa linapambuka m'njira, Ndi mtima wanga unatsata maso anga? Ngati cirema camamatira manja anga?