Job 31:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Ngati mtima wanga udanyengedwapo ndi mkazi, ndipo ngati ndidalalira pa khomo la mnansi wanga,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ngati mtima wanga wakopeka ndi mkazi, ngati ndalalira pa khomo la mnzanga,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ngati mtima wanga unakopekapo ndi mkazi, ndipo ngati ndinalakalaka mkazi wa mnansi wanga,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati mtima wanga wakopeka ndi mkazi, Ngati ndalalira pa khomo la mnzanga,