Job 32:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono anthu atatu aja adaleka osamulankhuzanso Yobe, chifukwa choti iyeyo adaadziwona kuti ndi wosachimwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamenepo amuna atatuwa analeka kumyankha Yobu; pakuti anali wolungama pamaso pake pa iye mwini.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono anthu atatuwa analeka kumuyankha Yobu, chifukwa chakuti iyeyo ankadziona kuti ndi wolungama.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamenepo amuna atatuwa analeka kumyankha Yobu; pakuti anali wolungama pamaso pace pa iye mwini.