Job 32:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Zoona, ndinkadikira mau anuwo, ndinkafuna kumvetsera mau ogwira mtima pamene inuyo munkafunafuna zanzeru zoti mulankhule.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, ndinalindira mau anu, ndinatcherera khutu zifukwa zanu, pofunafuna inu ponena.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndadikira nthawi yonseyi, ndimamvetsera mwachidwi zimene mumayankhula, pamene mumafunafuna mawu oti muyankhule,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani, ndinalindira mau anu, Ndinacherera khutu zifukwa zanu, Pofunafuna inu ponena.