Job 32:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yobe sadalankhule ndi ine, ndipo ine sindimuyankha monga m'mene mwamuyankhira inu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
popeza sanandiponyere ine mau, sindidzamyankha ndi maneno anu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Yobu sanayankhule motsutsana ndi ine, ndipo ine sindimuyankha monga mmene inu mwamuyankhira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Popeza sanandiponyera ine mau, Sindidzamyankha ndi maneno anu.