Job 32:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti ndili nawo mau ambiri, mtima wanga ukundichichiza kuti ndilankhule.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ndadzazidwa ndi mau, ndi mzimu wa m'kati mwanga undifulumiza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti ndili nawo mawu ambiri, ndipo mtima wanga ukundikakamiza;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ndadzazidwa ndi mau, Ndi mzimu wa m'kati mwanga undifulumiza.