Job 32:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndithudi, maganizo adzaza mumtima mwanga ali ngati vinyo wopanda pompungulira, ineyo ndili ngati matumba atsopano achikopa ofuna kuphulika ndi vinyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, m'chifuwa mwanga muli ngati vinyo wosowa popungulira, ngati matumba atsopano akuti aphulike.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
mʼkati mwanga ndili ngati botolo lodzaza ndi vinyo, ngati matumba a vinyo watsopano amene ali pafupi kuphulika.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani, m'cifuwa mwanga muli ngati vinyo wosowa popungulira, Ngati matumba atsopano akuti aphulike.