Job 32:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adapseranso mtima abwenzi ake atatu aja, chifukwa choti sadathe kuyankha, ngakhale iwo omwe adaapeza kuti Yobeyo ndi wolakwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adapsa mtima pa mabwenzi ake atatu omwe, pakuti anasowa pomyankha; koma anamtsutsa Yobu kuti ali woipa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anapseranso mtima abwenzi ake atatu aja chifukwa sanapeze njira yomutsutsira Yobu, ngakhale iwo anamupeza kuti anali wolakwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adapsa mtima pa mabwenzi ace atatu omwe, pakuti anasowa pomyankha; koma anamtsutsa Yobu kuti ali woipa.