Job 32:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Elihu adadikira kuti alankhule ndi Yobe, chifukwa choti abwenziwo anali akuluakulu kupambana iyeyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Elihu analindira kulankhula ndi Yobu, popeza akulu misinkhu ndi iwowa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Elihu anadikira kuti ayankhule ndi Yobu chifukwa choti abwenziwo anali akuluakulu kupambana iyeyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Elihu analindira kulankhula ndi Yobu, popeza akulu misinkhu ndi iwowa.