Job 32:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndinkati ayambe ndi akuluakulu aja kulankhula, chifukwa amvulazakale ndiwo amaphunzitsa nzeru.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinati, Amisinkhu anene, ndi a zaka zochuluka alangize nzeru.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndimaganiza kuti, ‘Ayambe ndi akuluakulu kuyankhula; anthu amvulazakale ndiwo amaphunzitsa nzeru.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinati, Amisinkhu anene, Ndi a zaka zocuruka alangize nzeru.