Job 32:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma mzimu wa Mphambe ndiwo umaloŵa mwa anthu ndi kuŵapatsa nzeru.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma m'munthu muli mzimu, ndi mpweya wa Wamphamvuyonse wawazindikiritsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma mzimu wa Mulungu mwa munthu, mpweya wa Wamphamvuzonse, ndi umene umapereka nzeru zomvetsa zinthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma m'munthu muli mzimu, Ndi mpweya wa Wamphamvuyonse wawazindikiritsa.