Job 32:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sikuti ukalamba wokha ndiwo umasandutsa anthu kuti akhale anzeru, si kukhwima kokha kumene kumachititsa kuti anthu azimvetsa zimene zili zoyenera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akulu sindiwo eni nzeru, ndi okalamba sindiwo ozindikira chiweruzo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Si okalamba amene ali ndi nzeru, si amvulazakale okha amene ali ndi nzeru zomvetsa zinthu zimene zili zoyenera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akulu sindiwo eni nzeru, Ndi okalamba sindiwo ozindikira ciweruzo.