Job 33:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Inu aYobe simukukhoza pa zimenezi, popeza kuti Mulungu ndi wamkulu kupambana munthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, ndidzakuyankhani m'mene muli mosalungama; pakuti Mulungu ndiye wamkulu woposa munthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Koma ine ndi kuti kwa inu, inuyo simukukhoza pa zimenezi, pakuti Mulungu ndi wamkulu kupambana munthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani, ndidzakuyankhani m'mene muli mosalungama; Pakuti Mulungu ndiye wamkulu woposa munthu.