Job 33:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa chiyani mukulimbana ndi Mulungu nkumanena kuti, ‘Pa mau angaŵa sadzayankhapo ndi amodzi omwe?’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mutsutsana ndi Iye chifukwa ninji? Popeza pa zake zonse sawulula chifukwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa chiyani mukudandaula kwa Iye kuti sayankha mawu ena aliwonse a munthu?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mutsutsana ndi Iye cifukwa ninji? Popeza pa zace zonse saulula cifukwa.