Job 33:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu amachita izi kuti amletse munthu zoipa zimene amachita, amafuna kuthetseratu kunyada kwake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti achotse munthu ku chimene akadachita, ndi kubisira munthu kudzikuza kwake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kumuchotsa munthu ku zoyipa, ndi kuthetseratu kunyada kwake,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuti acotse munthu ku cimene akadacita, Ndi kubisira munthu kudzikuza kwace;