Job 33:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mwina Mulungu amalanganso munthu ndi matenda kuti akonzeke, nthaŵiyo thupi lake lonse limangophwanya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Alangidwanso ndi zowawa pakama pake, ndi kulimbana kowawa kosapuma m'mafupa ake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Mwina Mulungu amalanga munthu ndi matenda ndi ululu ali pa bedi pake, nthawiyo thupi lake lonse limangophwanya,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Alangidwanso ndi zowawa pakama pace, Ndi kulimbana kowawa kosapuma m'mafupa ace.