Job 33:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthuyo akutsikira ku manda, ali pafupi kupita ku malo a anthu akufa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Inde wasendera kufupi kumanda, ndi moyo wake kwa akuononga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthuyo amayandikira ku manda, moyo wake umayandikira kwa amene amabweretsa imfa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Inde wasendera kufupi ku manda, Ndi moyo wace kwa akuononga.